Amidu Monjeza - Mudikirebe: (The Trending Song In Malawi)
| | |

Amidu Monjeza – Mudikirebe: (The Trending Song In Malawi)

Amidu Monjeza – Mudikirebe: (The Trending Song In Malawi).
Its three in the morning, ndazuka ndichitulo
Ndiwerenge then ndikalowe nkalasi at seven
Eya ndasambira safu kuno Breakfast abale kulibe kuno
Kuyimbira fone kunyumba kungopereka moni, akuti sizinthu sizilibwino kuno
Ati Helo mwanawe tikudziwa suli bho, Koma kunonso zinthu nde sizikuyenda
Tungokhalira madeya, fungo la mgaiwa tumvera kwa aneba

Amidu Monjeza – Mudikirebe: (The Trending Song In Malawi)

https://www.youtube.com/watch?v=uOSvoShzM6Y

Ndeno Udikirebe, komanso tipempherebe
Wakumwamba amadyesa njiwa ndi mileme
Ndeno kukusiya sizingatheke
Ndati ulimbikirebe, komanso tipempherebe
Wakumwamba amadyesa njiwa ndi mileme
Nde kukusiya sizingatheke

Kunjirako Muziyenda oliko Muziyenda
Poti tili pa mtunda pa mtunda komabe taziyenda
Kutsogoloko kuli nsetse mwanawe ndiyeno kaziyenda

Ukumana ndizokhoma, moyo wako suku umva kukoma
Uli ndi Degree sizikuyenda nzako kusangalala everyday koma alibe olo Diploma
Yes thats how life goes on umphunzire dziko just carry on osadodoma
Pena ukapunthwa lirapo eya siiwe Robot koma osaima my dear
Muli ma ups and down njiramu muli miyala muli minga muli njoka
Ma ups and down oh my god miyala minga komanso njoka

Ndeno Udikirebe, komanso tipempherebe
Wakumwamba amadyesa nyama ndi mileme
Ndeno kukusiya sizingatheke
Ndati ulimbikirebe, komanso tipempherebe
Wakumwamba amadyesa njiwa ndi mileme
Nde kukusiya sizingatheke

Download and Stream Amidu Monjeza below

Amidu Monjeza – Mudikirebe: (The Trending Song In Malawi)
Amidu Monjeza – Mudikirebe: (The Trending Song In Malawi)

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *